zambiri za ife

ntchito zanthu

    • kulandira ndi kufufuza madandaulo okhudza a polisi ngati anthu kapena polisi ngati bungwe.
    • kufufuza imfa kapena kuvulala kamba ka kagwiridwe ntchito ka apolisi
    • kufufuza imfa kapena kuvulala munthu ali m'manja mwa a apolisi
    • kulangiza aku mipando oyenelera kudzela mu zotsatila za kafufuku wathu.
ny-MWChichewa