zambiri za ife

ndife ndani

The Independent Complaints Commission (ICC) ndi nthambi ya boma yoziyimila payonkha yomwe ina khazikitsidwa, ndi malamulo oyendetsa ntchito za polisi ndi cholinga cholimbikitsa a polisi kutsata ndi kulemekeza malamulo pamene akugwira ntchito yawo. ICC inakhazikitsidwa m'malamulo mu 2010, inayamba ntchito yake mu ogasiti chaka cha 2021 

masomphenya a ICC  

bungwe loziyimila palokha, lomwe limalimbikitsa a Malawi polisi kulemekeza ufulu wachibadwidwe komaso kugwira ntchito mwa ukadaulo.

cholinga cha ICC

kuwonetsetsa kuti a polisi akugwira ntchito yawo molemekeza mamulo, ndipo tizachita izi, moyima patokha, posayang'ana nkhope komanso mwaukadaulo mu kafukufuku wathu, ndi cholinga chofuna kupititsa patsogolo chikhulupiliro cha anthu mwa a polisi.  

Motto

Promoting professional and rights-based policing.   

Our Values

Independence

We are guided by law and evidence.

Integrity

We are accountable, transparent, and consistent. 

Impartiality

We execute our duties objectively and without fear or favor.  

Trust

We are dependable, open, and courteous. 

Partners

ny-MWChichewa